Mfundo ya Kumapeto
^ [1] (ndime 9) Kuti muone zitsanzo za mmene Mboni za Yehova zinaonetsela cikondi kwa abale ao panthawi ya ngozi zacilengedwe, ŵelengani Nsanja ya Olonda ya July 15, 2002 tsa. 8-9, ndi buku lakuti Jehovah’s Witnesses—Proclaimers of God’s Kingdom, nkhani 19.