Mawu Amunsi
c “Zamalisece” zimene zachulidwa pano ndi zinthu monga zithunzithunzi, mabuku, ndi mau a pafoni odzutsa cilakolako cakugonana. Zamalisece zimaphatikizapo cithunzithunzi ca munthu amene waima modzutsa cilakolako ca kugonana, kapena zithunzithunzi za anthu aŵili kapena oposelapo amene akugonana.