Mawu Amunsi
c M’Malemba, mau akuti “zinthu zodetsa” amaphatikizapo macimo ambili. Ngakhale kuti si zodetsa zonse zimene zimafunikila komiti ya ciweluzo, munthu angacotsedwe mumpingo ngati mosalapa apitiliza kucita khalidwe lodetsa kwambili.—2 Akorinto 12:21; Aefeso 4:19; onani “Mafunso Ocokela kwa Owelenga” mu Nsanja ya Olonda ya July 15, 2006.