Mawu Amunsi
b Malinga ndi kaŵelengedwe ka nthawi m’Baibulo ndiponso mbili yakale, Yesu ayenela kuti anabadwa mu 2 B.C.E. mwezi wa Ciyuda wochedwa Etanimu, umene mogwilizana ndi kalendala yathu ndi pakati pa September ndi October.—Onani buku la Insight on the Scriptures, Voliyamu 2, patsamba 56 mpaka 57, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.