Mawu Amunsi
e Eostre (kapena kuti Eastre) analinso mulungu wamkazi wa kubeleka. Malinga ndi dikishonale ina, “iye anali ndi kalulu ku mwezi amene anali kukonda mazila ndipo nthawi zina anali kumujambula ali ndi mutu ngati wa kalulu.”—The Dictionary of Mythology.