Mawu Amunsi c Gulu loyamba la odzozedwa amene ali mbali ya “m’badwo uwu” ndi Akristu amene anaona “ciyambi ca masautso” mu 1914. Aliyense amene anadzozedwa pambuyo pakuti odzozedwa onse a m’gulu loyambali afa, sali mbali ya “m’badwo uwu.”—Mat. 24:8.