Mawu Amunsi
d Kuti mumve za kamvedwe katsopano kameneka, onani Nsanja ya Olonda ya October 15, 1995, patsamba 23 mpaka 28; January 15, 2008, patsamba 20-24; July 15, 2008, patsamba 17 mpaka 21, ndi Nsanja ya Mlonda ya July 1, 2013, patsamba 15 mpaka 20.