Mawu Amunsi
c Mu June caka ca 1880, magazini ya Zion’s Watch Tower inanena kuti anthu a 144,000 ndi Ayuda amene adzakhala Akristu pofika caka ca 1914. Koma cakumapeto kwa caka ca 1880, nkhani ina inafalitsidwa imene inafotokoza bwino za anthu amenewa, ndipo mfundo zake sizinasinthe mpaka panthawi ino.