Mawu Amunsi
c Panthawiyo, abale mumpingo anali kuvota kuti asankhe akulu. Motelo abale akanasankha kusavotela anthu mumpingo amene sanali kufuna kugwila nchito yolalikila. M’Nkhani 12, tidzakambilana mmene zinthu zinasinthila kuti akulu ayambe kuikidwa mwa kukwanilitsa ziyeneletso za m’Malemba.