Mawu Amunsi
a M’zipembedzo zina amanena kuti kuchula dzina la Mulungu, ngakhale popemphela, n’kulakwa. Koma dzina limenelo limapezeka maulendo pafupifupi 7,000 m’zinenelo zoyambilila za Baibo. Kawili-kawili dzinali imapezeka m’mapemphelo na mu nyimbo zotamanda Mulungu za atumiki okhulupilika a Yehova.