Mawu Amunsi
b M’nthawi za m’Baibulo, cikwati ca pacilamu, kapena kuloŵa cokolo, unali mwambo wakuti mwamuna akwatile mkazi wa m’bale wake wopanda ana, kuti abeleke ana ndi colinga cakuti dzina la banja la m’bale wake lisafafanizike.—Gen. 38:8; Deut. 25:5, 6.