Mawu Amunsi
c Aja amene adzaukitsidwa padziko lapansi, adzakhala ndi ciyembekezo ca moyo wosatha, osati moyo wosafa. Kuti mudziŵe zambili ponena za kusiyana pakati pa moyo wosafa ndi moyo wosatha, onani Nsanja ya Olonda yacingelezi ya April 1, 1984, masamba 30-31..