Mawu Amunsi
b Kuti mapemphelo athu akhale ovomelezeka kwa Mulungu, tiyenela kuyesetsa kucita zinthu mogwilizana ndi zofuna zake. Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani 17 m’buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni