Mawu Amunsi
a Ngakhale kuti okwatilana angakhululukilane ndi kuthetsa mavuto m’banja lao, Baibulo limakamba kuti mwamuna kapena mkazi wosalakwayo ali ndi ufulu wosankha kaya kukhululukila kapena kuthetsa cikwati ndi mnzake amene wacita cigololo. (Mat. 19:9) Onani nkhani yakuti “Lingaliro la Baibulo: Chigololo—Kukhululukira Kapena Kusakhululukira?” mu Galamukani! ya August 8, 1995.