Mawu Amunsi
a Matendawa amachedwa kuti cerebral palsy (CP). Dzinali amaligwilitsila nchito kuchula matenda okhudza ubongo amene amalepheletsa munthu kuyenda ndi kucita zinthu zina. Amacititsanso munthu kukunyuka, kulephela kudya, ndi kuvutika kulankhula. Matendawa amaopsa kwambili akakhudza manja ndi miyendo cifukwa zimenezi zimacititsa kuti ziwalozo zisamagwile nchito ndipo khosi limauma.