Mawu Amunsi
a M’fanizo limeneli, pali nyengo ya nthawi kucokela pamene mau akuti “Mkwati uja wafika!” akumveka (vesi 6) ndi kubwela kapena kufika kwa mkwati (vesi 10). M’masiku otsiliza ano, odzozedwa apitilizabe kukhala maso. Iwo aona cizindikilo ca kukhalapo kwa Yesu, ndipo akudziŵa kuti iye akulamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Ngakhale zili conco, io afunika kukhalabe maso mpaka iye atabwela kapena kufika.