Mawu Amunsi
a Nsanja ya Mlonda ya July 1, 2013, tsamba 28, ndime 8-10 inafotokoza yemwe ali kapolo wokhulupilika ndi wanzelu. Nkhani yapita m’magazini ino inafotokoza kuti anamwali amaimila ndani. Fanizo la nkhosa ndi mbuzi linafotokozedwa mu Nsanja ya Olonda ya October 15, 1995, tsamba 23 mpaka 28 ndiponso mu nkhani yotsatila m’magazini ino.