Mawu Amunsi
d Pambuyo poti atumwi afa, mpatuko unafalikila mumipingo yonse. Kwa zaka zambili, nchito yolalikila sinali kugwilidwa mwakhama. Koma mkati mwa nthawi “yokolola” kapena kuti nthawi ya mapeto, nchito yolalikila inali kudzayambanso kugwilidwa mwakhama. (Mat. 13:24-30, 36-43) Onani Nsanja ya Mlonda ya July 1, 2013, tsamba 15-18.