Mawu Amunsi
a Nkhani ino ndiponso yotsatila zalembedwela makamaka akulu. Koma nkhanizi zikhudza onse mumpingo. N’cifukwa ciani tikutelo? Cifukwa zidzathandiza abale onse obatizidwa kudziŵa kuti afunika kuphunzitsidwa kuti azisamalila maudindo mumpingo. Ndipo abale ambili akakhala paudindo, aliyense mumpingo amapindula.