Mawu Amunsi
a Ngati m’bale wacinyamata akuonetsa kukula mwakuuzimu, ndipo ndi wodzicepetsa komanso akukwanilitsa ziyeneletso zina za m’Malemba, akulu angamuyamikile kuti aikidwe kukhala mtumiki wothandiza ngakhale kuti sanakwanitse zaka 20 zakubadwa.—1 Tim. 3:8-10, 12; onani Nsanja ya Olonda ya July 1, 1989, tsamba 29.