Mawu Amunsi
a Ubwenzi umatanthauza mmene anthu aŵili amamvelela akamaganizilana ndiponso mmene amacitila zinthu kwa wina ndi mnzake. Conco, onse aŵili amafunika kucitapo kanthu kuti ubwenzi ukhalepo.