Mawu Amunsi
b Nyimbo ya Debora ikuonetsa kuti Sisera anali kubwela ndi akazi ambili kucokela kunkhondo ndipo nthawi zina anali kubweletsela m’silikali aliyense akazi aŵili kapena atatu. (Oweruza 5:30) Mau akuti “mkazi” pa lemba limeneli akutanthauza “mimba.” Mauwa akuonetsa kuti akazi amenewa anali kugwililidwa.