Mawu Amunsi
a Paulo anapempha Timoteyo kuti adulidwe, ndipo iye anavomeleza, osati cifukwa cakuti cinali ciyeneletso kwa Akristu, koma cifukwa cakuti Paulo sanafune kuti Ayuda amene anali kuwalalikila azimutsutsa cifukwa coyenda ndi mnyamata amene atate ake anali munthu wakunja.—Machitidwe 16:3.