Mawu Amunsi
a Mwana wa Abulahamu, Isaki, nayenso anakhala ndi cisoni kwa nthawi yaitali. Malinga ndi zimene zili m’nkhani yakuti “Tengelani Cikhulupililo Cao” imene ili mu Nsanja ya Mlonda ino, Isaki analila amai ake kwa zaka zitatu.—Genesis 24:67.