Mawu Amunsi
b Malingalilo okhudza kugwila nchitoyi anapelekedwa m’buku lakuti Millennial Dawn Volume 6 (1904) ndi m’magazini ya Zion’s Watch Tower ya August 1906, ya m’Cijelemani. Magazini ya The Watch Tower ya September 1915, inasintha kamvedwe ka mfundo imeneyo, ndipo inafotokoza kuti Ophunzila Baibulo ayenela kupewelatu kuloŵa usilikali. Koma nkhani imeneyi munalibe m’magazini ya Cijelemani.