Mawu Amunsi
a Katswili wina, James Parkes, analemba kuti: “Ayuda . . . anali kuloledwa kucita miyambo yawo. Panalibe ciliconse capadela copelekela ufulu wotelo kwa Ayuda. Mwa kucita zimenezi, Aroma anali kutsatila mwambo wawo. Anali na mphamvu zopatsa munthu aliyense wa m’dziko lawo ciliconse cimene iwo afuna.”