Mawu Amunsi
a Baseball ni maseŵela a bola amene matimu aŵili amapikisana. Timu iliyonse imakhala ndi anthu 9. Munthu mmodzi wa timu ina amaponya bola ndipo wa timu ina amayesa kumenya bolayo ndi ndodo yomenyela.