Mawu Amunsi
b Mwacionekele, akatswili ena anali atafalitsapo kale Baibo ya Cipangano Catsopano yomasulidwa m’Ciheberi. Mmodzi wa iwo anali Simon Atoumanos, wansembe amene anakhalako mu ulamulilo wa Byzantine m’zaka za m’ma 1360. Wina anali Oswald Schreckenfuchs, katswili wa ku German wa m’zaka za m’ma 1565. Mabaibo amenewa sanafalitsidwe ndipo sangapezeke.