Mawu Amunsi
a Mu alifabeti ya Cigiriki, kacilembo kocepetsetsa ni iota. Mwacionekele kacilembo aka kalinganako na kaciheberi י (yod). Popeza Cilamulo ca Mose cinalembedwa m’Ciheberi, Yesu ayenela kuti anali kukamba za kacilembo kaciheberi.