Mawu Amunsi
a Mwanda umodzi ni 10,000. Ndipo mwanda umodzi kuculukitsa ndi mwanda umodzi timapeza 100 miliyoni. Komabe, lemba la Chivumbulutso limakamba za “miyanda kuculukitsa ndi miyanda” ya angelo. Izi zikutanthauza mamiliyoni mahandiledi ambili, ngakhalenso mabiliyoni, a zolengedwa zauzimu!