Mawu Amunsi
b Kwa kanthawi, Yehova analola anthu kukwatila mphali komanso kukhala na zisumbali. Koma pambuyo pake anapatsa Yesu Khristu mphamvu yolamula kuti ukwati uzikhala wa mwamuna mmodzi na mkazi mmodzi, monga mmene zinalili poyamba mu Edeni.—Genesis 2:24; Mateyu 19:3-9.