Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, mau akuti “anthu othaŵa kwawo” amene taseŵenzetsa akutanthauza anthu amene akakamizika kuthaŵa n’kukakhala m’dziko lina kapena m’dela lina m’dziko lawo lomwelo cifukwa ca nkhondo, kuzunzidwa, kapena masoka. Bungwe la UNHCR (United Nations High Commissioner for Refugees) linati masiku ano, “munthu mmodzi pa anthu 113” padziko lonse “ni wothaŵa kwawo.”