Mawu Amunsi
a Mau a m’zinenelo zoyambilila za Baibo akuti Sheol ndi Hades amatanthauza manda a anthu onse. Koma m’Mabaibo ena, mau amenewa anawamasulila kuti “helo.”