Mawu Amunsi
b Pofuna kutikonzekeletsa kuimba, cigawo ciliconse pa msonkhano wacigawo kapena wadela cimayamba na mbali ya mamineti 10 ya nyimbo. Nyimbo zimenezi zimakonzewa m’njila yakuti zitithandize kukonzekeletsa mitima na maganizo athu kaamba ka pulogilamu ya msonkhano. Conco, tikulimbikitsidwa kuti nthawi ikakwana, tizikhala pansi na kumvetsela mwachelu nyimbozi.