Mawu Amunsi
a Buku lofalitsidwa na bungwe lina la zaumoyo ku Britain linati: “Ma IUD okhala na kopa yambili ni odalilika ngako cakuti ciŵelengelo ca azimayi amene satenga mimba ngati amaseŵenzetsa njilayi cimapitilila 99 pelesenti. Izi zitanthauza kuti ciŵelengelo ca azimayi amene angatenge mimba pa caka ngati aseŵenzetsa ma IUD aconco sicifika ngakhale 1 pelesenti. Koma ma IUD okhala na kopa yocepa, amakhalanso ocepelako mphamvu.”—England’s National Health Service.