Mawu Amunsi
a Mfundo zothandiza pophunzila buku lakuti “Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni” ni cida camphamvu cimene cingathandize acicepele na acikulile. Mfundo zimenezi zingawathandize kumvetsetsa coonadi ca m’Baibo na kudziŵa mmene angaphunzitsileko ena. Mfundo zimenezi zilipo m’zitundu zosiyana-siyana pa webusaiti yathu. Pitani pa peji ya Chichewa ya jw.org, na kuona pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA >ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA BAIBULO.