Mawu Amunsi
b Mboni za Yehova zimaphunzitsa anthu Baibo mahala. Zingakuthandizeni kuti muzimvetsetsa Malemba. Kuti mudziŵe mmene izi zimacitikila, tambani vidiyo yakuti, Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? Mungaipeze pa jw.org, mwa kulemba dzina la vidiyo imeneyi pa malo ofufuzila.