Mawu Amunsi
a Azimayi amene amavutika maganizo akabeleka, cimawavuta kuti aonetse cikondi kwa khanda lawo. Koma sayenela kudziimba mlandu kuti iwo ndiwo ali na vuto. Malinga na zimene inakamba Bungwe la U.S. National Institute of Mental Health, kuvutika maganizo “kumabwela cifukwa ca zocitika zina zakuthupi komanso zokhudza maganizo, . . . koma sikuti pali zimene mayi amacita kapena kulephela kucita.” Kuti mudziŵe zambili pa nkhani imeneyi ŵelengani nkhani yakuti, “Ndinagonjetsa Vuto Langa Losokonezeka Maganizo Nditabereka” mu Galamukani! ya Chichewa ya August 8, 2002.