Mawu Amunsi
b Sukuluyi manje inaloŵedwa m’malo na Sukulu ya Alengezi a Ufumu. Atumiki a nthawi zonse amene akutumikila ku dziko lina, ndipo ni oyenelela kuloŵa sukuluyi malinga na ziyenelezo, angafunsile kuti akaloŵe sukuluyi m’dziko lawo kapena ku dziko lina, kumene imacitikila m’citundu cawo.