Mawu Amunsi
a Liu la Cigiriki limene linamasulidwa kuti “onenela anzawo zoipa,” kapena kuti “woneneza” ni di·aʹbo·los. M’Baibo, liu limeneli limagwilitsidwa nchito monga dzina la Satana, amene amanenela Mulungu zoipa.