Mawu Amunsi
b Atate ake a Nowa, a Lameki, amenenso anali munthu woopa Mulungu, anafa kutatsala zaka zisanu kuti Cigumula cicitike. Ngati amayi ake a Nowa na abululu ake anali moyo pamene Cigumula cinayamba, ndiye kuti anawonongedwa.