Mawu Amunsi
b N’cimodzi-modzi na Nowa. Nayenso anali na mkazi mmodzi, ngakhale kuti kukwatila cipali kunayamba kale-kale anthu atangopanduka kumene mu Edeni.—Gen. 4:19.