Mawu Amunsi
a Baibo imaonetsa kuti angelo ali na maina awo. (Ower. 13:18; Dan. 8:16; Luka 1:19; Chiv. 12:7) Popeza kuti Yehova anapatsa dzina nyenyezi iliyonse (Sal. 147:4), n’zosakayikitsa kuti angelo onse ali na maina, kuphatikizapo mngelo amene anakhala Satana.