Mawu Amunsi
a Liu lakuti “abale” lingaphatikizepo akazi mumpingo. Paulo anachula Akhristu a ku Roma amene anawalembela kalata kuti “abale.” Koma mwacionekele mu mpingowo munalinso alongo, ndipo ena anawachula maina awo. (Aroma 16:1, 3, 6, 12) Kwa nthawi yaitali, Nsanja ya Mlonda yakhala ikuchula Akhristu oona kuti ‘abale na alongo.’