Mawu Amunsi
a Kampasi ni kacipangizo kolingana na wochi yamivi, koma kamakhala na muvi umodzi wa magineti umene nthawi zonse umalata kumpoto. Ngati kacipangizo kameneka kamagwila bwino nchito kangathandize munthu kuti asasocele.