Mawu Amunsi
a Meriba uyu ni wina osati uja wa kufupi na ku Refidimu. Mosiyana ndi Meriba woyamba uja, Meriba waciŵiliyu anali kufupi na ku Kadesi, osati ku Masa. Komabe, madela onse aŵili anachedwa Meriba cifukwa ca mikangano imene inacitika kumeneko.—Onani mapu 7, pa peji 38, m’kabuku kakuti Buku Lothandiza Pophunzila Mau a Mulungu.