Mawu Amunsi
b Kuti mudziŵe mmene mungathetsele maganizo ofuna kudzipha, onani nkhani za mu Galamukani zakuti: “Kodi Kudzipha Ndi Njira Yabwino Yothetsera Mavuto?” (April 2014); “Kodi Mungatani Mukakhala ndi Maganizo Ofuna Kudzipha?” (January 2012); ndi yakuti “Moyo N’gokoma” (November 8, 2001).