Mawu Amunsi a Katswili wolemba mbili ya Ayuda, dzina lake Josephus, anakamba kuti Samueli anali na zaka 12 pa nthawiyo.