Mawu Amunsi
a Pa nthawi ina atatulutsidwa m’ndende, Yosefe anakamba kuti Yehova anamutonthoza pa mavuto ake mwa kum’patsa mwana wamwamuna. Iye anacha mwana wake woyamba dzina lakuti Manase, cifukwa anati: “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse.”—Gen. 41:51, ftn.