Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZA ZITHUNZI: Zithunzi zoonetsa mmene atumiki okhulupilika a Yehova anali kucitila Cikumbutso m’nthawi ya atumwi; cakumapeto kwa zaka za m’ma 1800; m’ndende yacibalo ya Nazi ku Germany; komanso m’Nyumba ya Ufumu yopanda zipupa ya m’nthawi yathu ino, m’dziko linalake la ku South America, kumene nyengo ni yotentha.